Song Cover Image

jhooo 2021.mp3 (Remix)

yooooo ‎Ndinee jhooo woziwika ‎Simiyone wochokela kusangaa ‎ ‎Dj Félix da f ‎ ‎ ‎kodi mufuna tikamadusana tizinshita kuwopa? ‎shomwe ine ndiziwilaa ulemo samashitta kupembha ayii ayii, kufasakuuu ‎sikupusa ayii Koma NDI ulemo, ‎muniveesse ‎ ‎ ‎akazatidalisa Malo anuwo tizakhalapo ndife ‎shomwe NDI ngaziwe inee mulungu amatikonda shomwe mungaziwe mbiyeee NDI wakulu, kuposa climanjaloo ‎ ‎ ‎ ‎kodi Inu bwana vutolano NDI Shani? mumalimbana ndife ana anghono ino ndino zotti zano zinayela kale komabe mukufuna muzilimbana nafe Kodi mufuna abale Anuu pa tawonipa azingomela unofuu? ‎ ‎ ‎akazatidalisa Malo anuwo tizakhalapo ndife ‎shomwe NDI ngaziwe inee mulungu amatikonda shomwe mungaziwe mbiyeee NDI wakulu, kuposa climanjaloo ‎ ‎ ‎ndikupeleka moni Kwa zizanga nose, ‎irmao JOAQUIM mukayaa, thokozani Chalosi, Jordão mwanapwa komaso mulamo wanga wayawaya alandile moni achambiyanga ‎ ‎achina m'kwate wakulu, komaso NDI ósse azimbiyanga alandile moni osayiwala achipwanya ‎ ‎ ‎chissaua on bit ‎niwala record ‎ ‎ ‎nyimboyi ndiyaye jhoo woziwika NDI Simiyone ‎ ‎akazii achipwanya mulandile ulemo nda achanawo OSE