
[Intro] Ndisanene fuck buddy Company sindingapange Ndisanene fuck buddy Company sindingapange [Chorus] Wandiuza wandisowa ndati ineso Koma ndi ineso sitingabweleranso Anzako Umawauza Umkandikonda ineso Koma ndi iweso Sindingayambileso Koma Ndisaname Mwina Titha kungokhala ma Fuck Buddies Utha Kumandikhola Ukafuna Company Koma Zobwelerana Nde singapange [Verse] Ndiku Dropa Tape 2 koma Album ili on The way Ndungofuna Ndingolowa chaku Nkhatabay or Capemaclear and put my Phone away I don’t know How, Buh i know i will find a way Nde tandipase plan Kuti ti linky Or ndingovunga location kuti ufike Ndukuvaisa ku Kitchen Kuti Uphike Kenako ukuziwa kale kuti ufile Kuvayisa pa bar kut u sippy Kuikora nyimbo kuti uvine Fe fr fr fr kuti ununkhile Zaza wezi Brain izungulire Kwinako ukuziwa kale zoti uchite Nde tasekeleratu usandilusire Wabwera utatchena koma tandivulire Another Round ima kaye ndikusutire [Chorus] Wandiuza wandisowa ndati ineso Koma ndi ineso sitingabweleranso Anzako Umawauza Umkandikonda ineso Koma ndi iweso Sindingayambileso Ndisaname Mwina Titha kungokhala ma Fuck Buddies Utha Kumandikhola Ukafuna Company Koma Zobwelerana Nde singapange Ndisaname Mwina Titha kungokhala ma Fuck Buddies Utha Kumandikhola Ukafuna Company Koma Zobwelerana Nde singapange [Post-Chorus] (Malawian) Ndisaname fuck buddy Company sindingapange Ndisaname fuck buddy Company sindingapange [Outro] Wandiuza wandisowa ndati ineso Koma ndi ineso sitingabweleranso Anzako Umawauza Umkandikonda ineso Koma ndi iweso Sindingayambileso Ndisaname Mwina Titha kungokhala ma Fuck Buddies Utha Kumandikhola Ukafuna Company Koma Zobwelerana Nde singapange Ndisaname Mwina Titha kungokhala ma Fuck Buddies Utha Kumandikhola Ukafuna Company Koma Zobwele

